[DOWNLOAD] "Momwe Mungakhalire Mkhristu Wamphamvu" by Dag Heward-Mills ~ eBook PDF Kindle ePub Free
eBook details
- Title: Momwe Mungakhalire Mkhristu Wamphamvu
- Author : Dag Heward-Mills
- Release Date : January 22, 2019
- Genre: Christianity,Books,Religion & Spirituality,
- Pages : * pages
- Size : 577 KB
Description
Mutalandira Yesu Khristu ngati Mbuye ndi Mpulumutsi wanu mumapulumutsidwa! Inu ndinu Mkhristu wobadwanso mwatsopano ndipo dzina lanu lalembedwa mu Bukhu la Moyo. Funso lanu ndilo: "Kodi sitepe yotsatira ndi yotani?" Pokhala Mkhristu ndi sitepe yabwino, koma ndi chiyambi chabe. Inu mukuyenera kukhala Mkhristu wabwino, wamphamvu. 'Nanga ndichita bwanji izi?' - M'buku ili labwino, mudzaphunzira njira zoti mutenge ndikukhala Mkhristu wamphamvu yemwe ali wokonzeka kufa kapena mkwatulo.